Romans 11:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Momwemonso Ayuda tsopano samvera Mulungu, koma cholinga chake nchakuti iwonso adzalandire chifundo pa nthaŵi yake, chifukwa cha chifundo mwalandira inuchi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
choteronso iwo sanamvera tsopano, kuti iwonso akalandire chifundo, chifukwa cha chifundo cha kwa inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chonchonso iwo akhala osamvera tsopano kuti iwonso alandire chifundo chifukwa cha chifundo cha Mulungu kwa inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
coteronso iwo sanamvera tsopano, kuti iwonso akalandire cifundo, cifukwa ca cifundo ca kwa inu.