Romans 11:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Mulungu adamuyankha chiyani? Adati, “Ndadzisungira anthu zikwi zisanu ndi ziŵiri amene sadapembedzepo Baala, mulungu wonama uja.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kuyankha kwa Mulungu kudatani kwa iye? Ndinadzisiyira ndekha anthu amuna zikwi zisanu ndi ziwiri, amene sanagwadira Baala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo yankho la Mulungu linali lotani? “Ine ndadzisungira ndekha anthu 7,000 amene sanapembedzepo Baala.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kuyankha kwa Mulungu kudatani kwa iye? Ndinadzisiyira ndekha anthu amunazikwi zisanu ndi ziwiri, amene sanagwadira Baala.