Romans 11:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bwanji tsono? Aisraele sadapeze zimene ankafunafuna. Koma anthu pang'ono chabe amene Mulungu adaŵasankha ndiwo adazipeza. Otsalawo adagontha m'khutu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chiyani tsono? Ichi chimene Israele afunafuna sanachipeza; koma osankhidwawo anachipeza, ndipo otsalawo anaumitsidwa mtima;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchiyani tsopano? Chimene Aisraeli anachifuna ndi mtima wonse sanachipeze koma osankhidwawo anachipeza. Enawo anawumitsidwa mtima
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ciani tsono? ici cimene Israyeli afunafuna sanacipeza; koma osankhidwawo anacipeza, ndipo otsalawo anaumitsidwa mtima;