Romans 11:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
monga Malembo anenera kuti, “Mulungu adaŵapatsa mtima wosatha kumvetsa zinthu, ndipo mpaka lero lino waŵasandutsa osatha kupenya ndi osatha kumva.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
monga kunalembedwa kuti, Mulungu anawapatsa mzimu watulo, maso kuti asapenye, ndi makutu kuti asamve, kufikira lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
monga kwalembedwa kuti, “Mulungu anawapatsa mzimu wosatha kumvetsa zinthu, maso osatha kupenya; makutu osatha kumva mpaka lero lino.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
monga kunalembedwa kuti, Mulungu anawapatsa mzimu watulo, maso kuti asapenye, ndi makutu kuti asamve, kufikira lero lino.