Romans 11:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Davide akuti, “Maphwando ao asanduke msampha ndi diŵa loŵakola, ndi kuŵagwetsa kuti alangidwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide akuti, Gome lao likhale kwa iwo, ngati msampha, ndi ngati diwa, ndi monga chokhumudwitsa, ndi chowabwezera chilango;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Davide akuti, “Maphwando awo asanduke msampha ndi diwa lowakola ndi chopunthwitsa kuti alandire chilango.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide akuti, Gome lao likhale kwa iwo, ngati msampha, ndi ngati diwa, Ndi monga cokhumudwitsa, ndi cowabwezera cilango;