Romans 13:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati munthu akonda mnzake, sangamchite choipa ai. Nchifukwa chake amene amakonda mnzake, wasunga zonse zimene Malamulo a Mulungu akunena.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chikondano sichichitira mnzake choipa; chotero chikondanocho chili chokwanitsa lamulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chikondi sichichitira mnzake zoyipa. Chifukwa chake chikondi ndicho chokwaniritsa lamulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cikondano sicicitira mnzace coipa; cotero cikondanoco ciri cokwanitsa lao mulo.