Romans 13:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndichonso mumakhomera msonkho: olamulira amatumikira Mulungu pamene akugwira ntchito yaoyi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti chifukwa cha ichi mupatsanso msonkho; pakuti iwo ndiwo atumiki a Mulungu akulabadirabe chinthu chimenechi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ichi nʼchifukwa chakenso inu mumapereka msonkho. Pakuti olamulira ndi atumiki a Mulungu amene amapereka nthawi yawo yonse kulamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti cifukwa ca ici mupatsanso msonkho; pakuti iwo ndi wo atumiki a Mulungu akulabadira be cinthu cimeneci.