Romans 14:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Malembo akunena kuti, “Ambuye akuti, ‘Pali Ine ndemwe, anthu onse adzandigwadira ndi kuvomereza kuti ndine Mulungu.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti kwalembedwa, Pali moyo wanga, ati Ambuye, mabondo onse adzagwadira Ine, ndipo malilime onse adzavomereza Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwalembedwa, akutero Ambuye, “Pamene Ine ndili ndi moyo, aliyense adzandigwadira ndipo lilime lililonse lidzavomereza Mulungu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti kwalembedwa, Pali moyo wanga, ari Ambuye, mabondo onse adzagwadira Ine, Ndipo malilime onse adzabvomereza Mulungu,