Romans 15:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiponso akuti, “Inu nonse a mitundu ina, tamandani Ambuye, anthu a mitundu yonse amtamande.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiponso, Tamandani Ambuye, inu a mitundu yonse; ndipo anthu onse amtamande.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo akutinso, “Tamandani Ambuye, inu nonse a mitundu ina, ndi kuyimba zotamanda Iye, inu anthu onse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiponso, Tamandani Ambuye, inu a mitundu yonse; Ndipo anthu onse amtamande.