Romans 15:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Malembo akuti “Anthu amene sadauzidwe za Iye, adzaona, amene sadamve za Iye, adzamvetsa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma monga kwalembedwa, Iwo amene uthenga wake sunawafikire, adzaona, ndipo iwo amene sanamve, adzadziwitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma monga kwalembedwa kuti, “Iwo amene sanawuzidwe za Iye adzaona, ndi iwo amene sanamve adzazindikira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma monga kwalembedwa, Iwo amene uthenga wace sunawafikire, adzaona, Ndipo iwo amene sanamve, adzadziwitsa.