Romans 15:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa chifukwa chimenechi ndidalephera kaŵirikaŵiri kufika kwanuko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chakenso ndinaletsedwa kawirikawiri kudza kwa inu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ichi nʼchifukwa chake ine ndakhala ndikuletsedwa kawirikawiri kubwera kwa inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cacenso ndinaletsedwa kawiri kawiri kudza kwa inu;