Romans 15:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zaka zambiri ndakhala ndikulakalaka kuti ndifike kumeneko. Ndipo tsopano, popeza kuti ndatsiriza ntchito yanga ku mbali zakuno,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma tsopano, pamene ndilibe malo m'maiko akuno, ndipo pokhala ndi kulakalaka zaka zambiri kudza kwa inu, ndidzatero,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma tsopano popeza kulibenso malo anga woti ndigwire ntchito mʼmadera awa, ndakhala ndikufuna kukuonani kwa zaka zambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma tsopano, pamene ndiribe malo m'maiko akuno, ndipo pokhala ndi kulakalaka zaka zambiri kudza kwa inu, ndidzatero,