Romans 15:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti Khristunso sankachita zinthu kungofuna kudzikondweretsa, koma ndi monga Malembo anenera kuti, “Chipongwe cha anthu okunyozani Inu chidafika pa Ine.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Khristunso sanadzikondweretsa yekha; koma monga kwalembedwa, Minyozo ya iwo amene anakunyoza iwe inagwa pa Ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ngakhale Khristu sanadzikondweretsa yekha koma, monga kwalembedwa kuti, “Chipongwe cha anthu okunyozani chinagwera Ine.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Kristunso sanadzikondweretsa yekha; koma monga kwalembedwa, Minyozo ya iwo amene anakuoyoza iwe Inagwa pa Ine,