Romans 16:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Moni kwa Rufu, wotchuka pa ntchito ya Ambuye. Moninso kwa mai wake amene ali ngati mai wanganso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Moni kwa Rufu, wosankhidwayo mwa Ambuye, ndi amai wake ndi wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Perekani moni kwa Rufo, wosankhidwa mwa Ambuye, ndi amayi ake, amene akhala amayi anganso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulankhule Rufo, wosankhidwayo mwa Ambuye, ndi amai wace ndi wanga.