Romans 16:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Timoteo, mnzanga wogwira naye ntchito, akukupatsani moni. Lusio, Yasoni ndi Sosipatere, Ayuda anzanga, nawonso akuti moni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Timoteo wantchito mnzanga akupatsani moni; ndi Lusio ndi Yasoni ndi Sosipatere, abale anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Timoteyo, mtumiki mnzanga, akupereka moni. Nawonso, Lusio, Yasoni ndi Sosipatro, abale anga akutero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Timoteo wanchito mnzanga akulankhulani inu; ndi Lukiyo ndi Yasoni ndi Sosipatro, abale anga.