Romans 16:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tsopano zatulukira poyera kudzera m'zimene aneneri adalemba, ndiponso kudzera m'lamulo la Mulungu wachikhalire zadziŵika kwa anthu a mitundu yonse, kuti azizikhulupirira ndi kuzimvera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma chaonetsedwa tsopano, ndi kudziwidwa kwa anthu a mitundu yonse mwa malembo a aneneriwo, monga mwa lamulo la Mulungu wosatha, kuti amvere chikhulupiriro;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma tsopano chavumbulutsidwa ndi kudziwika kudzera mʼMalemba a uneneri mwa lamulo la Mulungu wosatha, kuti mitundu yonse ikhulupirire ndi kumvera Iye,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
komai caonetsedwa tsopano, ndi kudziwidwa kwa anthu a mitundu yonse mwa malembo a aneneriwo, monga mwa lamulo la Mulungu wosatha, kuti amvere cikhulupiriro;