Romans 16:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwoŵa anali okonzeka kuphedwa kuti apulumutse moyo wanga. Si ndine ndekhatu ndikuŵathokoza, komanso mipingo yonse ya ku maiko a anthu a mitundu ina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene anapereka khosi lao chifukwa cha moyo wanga; amene ndiwayamika, si ine ndekha, komanso Mipingo yonse ya Ambuye ya kwa anthu amitundu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapereka miyoyo yawo chifukwa cha ine. Osati ine ndekha komanso mipingo yonse ya a mitundu ina ikuyamika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene anapereka khosi lao cifukwa ca moyo wanga; amene ndiwayamika, si ine ndekha, komanso Mipingo yonse ya Ambuye ya kwa anthu amitundu;