Romans 16:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Moni kwa Maria, amene wakhala akukugwirirani ntchito kolimba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Moni kwa Maria amene anadzilemetsa ndi ntchito zambiri zothandiza inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Perekani moni kwa Mariya, amene wakhala akukugwirirani ntchito kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulankhule Mariya amene anadzilemetsa ndi nchito zambiri zothandiza inu.