Romans 2:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mnzangawe amene umaweruza ena ochita zimenezi, pamene iwenso umachita zomwezo, kodi ukuganiza kuti chidzakuphonya chiweruzo cha Mulungu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo uganiza kodi, munthu iwe, amene umaweruza iwo akuchita zotere, ndipo uzichitanso iwe mwini, kuti udzapulumuka pa mlandu wa Mulungu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ukuganiza kuti udzathawa chiweruzo cha Mulungu iwe munthu wamba, pamene uweruza ena, iwe ndi kumachitanso zomwezo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo uganiza kodi, munthu iwe, amene umaweruza iwo akucita zotere, ndipo uzicitanso iwe mwini, kuti udzapulumuka pa mlandu wit Mulungu?