Romans 3:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'kamwa mwao m'moopsa ngati manda apululu, ndi lilime lao amalankhula zonyenga, pamilomo pao pamatuluka mau aululu, ululu wake wonga wa mamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mero mwao muli manda apululu; ndi lilime lao amanyenga; ululu wa mamba uli pansi pa milomo yao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kummero kwawo kuli ngati manda apululu; ndi lilime lawo amayankhula zachinyengo.” “Ululu wa mamba uli pa milomo yawo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mero mwao muli manda apululu; Ndi lilime lao amanyenga; Ululu wa mamba uli pansi pa milomo yao;