Romans 3:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amasakaza ndi kusautsa kulikonse kumene amapita,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kusakaza ndi kusauka kuli m'njira zao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kusakaza ndi chisoni kumaonekera mʼnjira zawo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kusakaza ndi kusauka kuli m'njira zao;