Romans 3:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pali phindu lalikulu ndithu kukhala Myuda. Choyamba, Mulungu adapatsa Ayuda mau ake kuti aŵasunge.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zambiri monsemonse: choyamba, kuti mau a Mulungu anaperekedwa kwa iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ubwino wake ndi wambiri mʼnjira zonse! Choyambirira iwo anapatsidwa Mawu a Mulungu kuti awasunge.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zambiri monse monse: coyamba, kuti mau a Mulungu anaperekedwa kwa iwo.