Romans 3:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kapena Mulungu ndi Mulungu wa Ayuda okha kodi? Suja alinso Mulungu wa anthu a mitundu ina? Ndithu ndiyenso Mulungu wa anthu a mitundu ina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kapena Mulungu ndiye wa Ayuda okhaokha kodi? Si wao wa amitundunso kodi? Eya, wa amitundunso:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi Mulungu ndi Mulungu wa Ayuda okha? Kodi si Mulungu wa a mitundu inanso? Inde wa a mitundu inanso,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kapena Mulungu ndiye wa Ayuda okha okha kodi? si wao wa amitundunso kodi? Bya, wa amitundunso: