Romans 3:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Mulungu ndi mmodzimodzi yemweyo, mwakuti pakukhulupirira, anthu oumbalidwa amapezeka kuti ngolungama pamaso pake, nawonso osaumbalidwa, pakukhulupirira amapezeka kuti ngolungama pamaso pa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngatitu ndiye Mulungu mmodzi, amene adzawayesa amdulidwe olungama ndi chikhulupiriro, ndi akusadulidwa mwa chikhulupiriro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
popeza ndi Mulungu mmodzi yemweyo amene adzalungamitsa mwachikhulupiriro ochita mdulidwe ndi osachita mdulidwe kudzera mʼchikhulupiriro chomwecho.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ngatitu ndiye Mulungu mmodzi, amene adzawayesa amdulidwe olungama ndi cikhulupiriro, ndi akusadulidwa mwa cikhulupiriro,