Romans 3:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ndiye kuti tikutaya Malamulo pamene tikunenetsa kuti pafunika chikhulupiriro? Mpang'ono pomwe. Makamaka tikuŵafikitsa pake penipeni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero kodi lamulo tiyesa chabe mwa chikhulupiriro? Msatero ai; koma tikhazikitsa lamulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi tsono ife, tikutaya Malamulo pamene tikunena kuti pafunika chikhulupiriro? Ayi. Mʼnjira iliyonse ayi! Komatu ife tikukwaniritsadi Malamulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero kodi lamulo tiyesa cabe mwa cikhulupiriro? Msatero ai; koma tikhazikitsa lamulo.