Romans 3:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma wina nkunena kuti, “Nanga kunama kwanga kutaonetsa koposa kale kuti Mulungu ndi woona, ndi kuwonjezera pa ulemu wake, kodi pamenepo angandiweruze kuti ndine wochimwa?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ngati choonadi cha Mulungu chichulukitsa ulemerero wake chifukwa cha bodza langa, nanga inenso ndiweruzidwa bwanji monga wochimwa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wina atanena kuti, “Ngati kunama kwanga kukuonetsa koposa kuti Mulungu ndi woona, ndi kuwonjezera pa ulemerero wake, nanga nʼchifukwa chiyani ndikuweruzidwa kuti ndine wochimwa?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ngati coonadi ca Mulungu cicurukitsa ulemerero wacecifukwa ca bodza langa, nanga inenso ndiweruzidwa bwanji monga wocimwa?