Romans 4:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono tinene chiyani za Abrahamu, kholo la ife Ayuda? Iyeyu adapezana ndi zotani?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsono tidzanena kuti Abrahamu, kholo lathu monga mwa thupi, analandira chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nanga tsono tidzati chiyani za Abrahamu kholo lathu, iyeyu anapezana ndi zotani pa nkhani imeneyi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsono tidzanena kuti Abrahamu, kholo lathu monga mwa thupi, analandira ciani?