Romans 4:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanga ndi liti zidachitika zimenezi? Kodi ndipo ataumbalidwa kapena asanaumbalidwe? Sizidachitike ataumbalidwa ai, koma asanaumbalidwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono chinawerengedwa bwanji? M'mene iye anali wodulidwa kapena wosadulidwa? Si wodulidwa ai, koma wosadulidwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi chinatengedwa bwanji? Kodi nʼkuti iye atachita mdulidwe kapena asanachite? Osati atachita mdulidwe koma asanachite!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono cinawerengedwa bwanji? m'mene iye anali wodulidwa kapena wosadulidwa? Si wodulidwa ai, koma wosadulidwa;