Romans 4:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuumbalidwako kudachitika pambuyo pake, kuti chikhale ngati chizindikiro chotsimikiza kuti asanaumbalidwe, adaapezeka kale kuti ngwolungama pamaso pa Mulungu pakukhululirira. Motero Abrahamu ndi kholo la onse okhulupirira Mulungu, ndipo Mulungu amaŵaona kuti ngolungama, ngakhale ndi osaumbalidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
iye ndipo analandira chizindikiro cha mdulidwe, ndicho chosindikiza chilungamo cha chikhulupiriro, chomwe iye anali nacho asanadulidwe; kuti kotero iye akhale kholo la onse akukhulupirira, angakhale iwo sanadulidwa, kuti chilungamo chiwerengedwe kwa iwonso;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iye anachita mdulidwe ngati chizindikiro ndi chitsimikizo cha kulungama kumene anali nako mwachikhulupiriro pomwe anali asanachite mdulidwe. Choncho, iye ndi kholo la onse amene akhulupirira koma sanachite mdulidwe, ndi cholinga chakuti alungamitsidwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo iye analandira cizindikilo ca mdulidwe, ndico cosindikiza cilungamo ca cikhulupiriro, comwe iye anali naco asanadulidwe; kuti kotero iye akhale kholo la onse akukhulupira, angakhale iwo sanadulidwa, kuti cilungamo ciwerengedwe kwa iwonso;