Romans 4:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiponso ndi kholo la onse oumbalidwa, osati okhawo amene adangoumbalidwa m'thupi mokha, komanso amene akutsata chitsanzo cha chikhulupiriro cha kholo lathu Abrahamu asanaumbalidwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndiponso kholo la mdulidwe wa iwo amene siali a mdulidwe okha, koma wa iwo amene atsata mayendedwe a chikhulupiriro chija cha kholo lathu Abrahamu, chimene iye anali nacho asanadulidwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iyenso ndiyenso kholo la ochita mdulidwe osati amene anangochita mdulidwe kokha koma amene amatsata chitsanzo cha chikhulupiriro chimene kholo lathu Abrahamu anali nacho asanachite mdulidwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndiponso kholo la mdulidwe wa iwo amene siali a mdulidwe okha, koma wa iwo amene atsata mayendedwe a cikhulupiriro cija ca kholo lathu Abrahamu, cimene iye anali naco asanadulidwe.