Romans 4:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati ndi odalira Malamulo okha amene adzalandire zimene Mulungu adalonjeza, ndiye kuti chikhulupiriro nchopanda pake, ndipo lonjezo lija lilibe phindu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ngati iwo a lamulo akhala olowa nyumba, pamenepo chikhulupiriro chayesedwa chabe, ndimo lonjezo layesedwa lopanda pake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ngati amene amadalira Malamulo ndiye olowa mʼmalo, ndiye kuti chikhulupiriro nʼchopanda pake ndipo lonjezano ndi lopanda phindu
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ngati iwo a lamulo akhala olowa nyumba, pamenepo cikhulupiriro eayesedwa cabe, ndimo lonjezo layesedwa lopanda pace;