Romans 4:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malamulo amangodzetsa chilango, koma kumene kulibe malamulo, kulibenso kuŵaphwanya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti chilamulo chichitira mkwiyo; koma pamene palibe lamulo, pamenepo palibe kulakwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa Malamulo anabweretsa chilango. Ndipo kumene kulibe Malamulo kulibenso kuwalakwitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti cilamulo cicitira mkwiyo; koma pamene palibe lamulo, pamenepo palibe kulakwa.