Romans 4:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Malembo akuti, “Ndakuika kuti ukhale kholo la mitundu yambiri ya anthu.” Lonjezo limeneli Abrahamu adalilandira kwa Mulungu mwini amene iye ankamukhulupirira. Ndi Mulungu amene amabwezera moyo kwa akufa, ndipo amapereka moyo kwa zinthu zopanda moyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
monga kwalembedwa: Ndinakukhazika iwe kholo la mitundu yambiri ya anthu pamaso pa Mulungu amene iye anamkhulupirira, amene apatsa akufa moyo, ndi kuitana zinthu zoti palibe, monga ngati zilipo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga kwalembedwa kuti, “Ine ndakusandutsa kukhala kholo la mitundu yambiri.” Iye ndiye kholo lathu pamaso pa Mulungu, amene anamukhulupirira, Mulungu amene amapereka moyo kwa akufa ndipo amapereka moyo kwa zinthu zopanda moyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
monga kwalembedwa: Ndinakukhazika iwe kholo la mitundu yambiri ya anthu pamaso pa Mulungu amene iye anamkhulupirira, amene apatsa akufa moyo, ndi kuitana zinthu zoti palibe, monga ngati ziripo,