Romans 4:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake, monga mau a Mulungu akunena, “Mulungu adamuwona kuti ngwolungama.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ichi chinawerengedwa kwa iye chilungamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake “chinamuchititsa kukhala wolungama.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ici cinawerengedwa kwa iye cilungamo.