Romans 4:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide adaanenanso zomwezo pamene adati ngwodala munthu amene Mulungu amuwona kuti ngwolungama popanda ntchito. Paja iye adanena kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monganso Davide anena za mdalitso wake wa munthu, amene Mulungu amwerengera chilungamo chopanda ntchito,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide ponena zomwezi pamene anayankhula za kudala kwa munthu amene Mulungu amulungamitsa osati chifukwa cha ntchito zake akuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monganso Davide anena za mdalitso wace wa munthu, amene Mulungu amwerengera cilungamo copanda nchito,