Romans 4:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ngodala anthu amene Mulungu adaŵakhululukira machimo ao, amene Iye adaŵafafanizira machimo ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuti, Odala iwo amene akhululukidwa kusaweruzika kwao, nakwiriridwa machimo ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Odala ndi amene zoyipa zawo zakhululukidwa; amene machimo awo afafanizidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuti, Odala iwo amene akhululukidwa kusayeruzika kwao, Nakwiriridwa macimo ao,