Romans 6:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono tinene chiyani? Kodi tinganene kuti tizingokhalabe mu uchimo kuti kukoma mtima kwa Mulungu kuchuluke?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake tidzatani? Tidzakhalabe m'uchimo kodi, kuti chisomo chichuluke?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nanga tinene chiyani? Kodi tipitirire kuchimwa kuti chisomo chichulukebe?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace tidzatani? Tidzakhalabe m'ucimo kodi, kuti cisomo cicuruke?