Romans 7:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abale, ndikulankhulatu ndi inu amene mumadziŵa za malamulo. Mukudziŵa bwino kuti malamulo amamkhudza munthu pokhapokha pamene munthuyo ali moyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanga kodi simudziwa, abale, pakuti ndilankhula ndi anthu akudziwa lamulo, kuti lamulolo lichita ufumu pa munthu nthawi zonse iye ali wamoyo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi simukudziwa abale kuti Malamulo ali ndi ulamuliro pa munthu pokhapokha ngati ali ndi moyo? Ine ndikuyankhula kwa anthu amene akudziwa Malamulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanga kodi simudziwa, abale, pakuti ndilankhula ndi anthu akudziwa lamulo, kuti lamulolo licita ufumu pa munthu nthawi zonse iye ali wamoyo?