Romans 7:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo ine ndidakhala ngati ndafa. Tsono malamulo omwewo amene adaayenera kufikitsa anthu ku moyo, ine adandifikitsa ku imfa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo lamulo, limene linali lakupatsa moyo, ndinalipeza lakupatsa imfa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo ine ndinafa. Ine ndinazindikira kuti Malamulo omwe ankayenera kubweretsa moyo anabweretsa imfa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo lamulo, limene linali Iakupatsa moyo, ndinalipeza lakupassa imfa.