Romans 7:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti uchimo udapeza mpata chifukwa cha malamulo, ndipo mwa malamulowo udandinyenga ndi kundipha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti uchimo, pamene unapeza chifukwa mwa lamulo, unandinyenga ine, ndi kundipha nalo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti uchimo unapeza mwayi chifukwa cha Malamulo ndipo kudzera mʼMalamulowo, unandinyenga ndi kundiyika mu imfa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ucimo, pamene unapeza cifukwa mwa lamulo, unandinyenga ine, ndi kundipha nalo.