Romans 7:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tikudziŵa kuti Malamulo a Mose ndi opatsidwa ndi Mulungu. Koma ine ndine munthu wofooka chabe, wogulitsidwa ngati kapolo ku uchimo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti tidziwa kuti chilamulo chili chauzimu; koma ine ndili wathupi, wogulitsidwa kapolo wa uchimo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife tikudziwa kuti Malamulo ndi auzimu; koma ine ndine munthu wofowoka chabe, wogulitsidwa ngati kapolo ku uchimo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti tidziwa kuti cilamulo ciri cauzimu; koma ine ndiri wathupi, wogulitsidwa kapolo wa ucimo.