Romans 7:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati sindifuna kuchita zoipa zimene ndimachita, ndiye kuti ndikuvomereza kuti Malamulo aja ndi abwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati ndichita chimene sindichifuna, ndivomerezana nacho chilamulo kuti chili chabwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ngati ndimachita zimene sindimafuna kuzichita, ndiye kuti ndikuvomereza kuti lamulo ndi labwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati ndicita cimene sindicifuna, ndibvomerezana naco cilamulo kuti ciri cabwino.