Romans 7:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero zimene zimachitikazo, sindine amene ndimazichita, koma uchimo umene umakhala mwa ine.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsopano si ine ndichichita, koma uchimo wakukhalabe m'kati mwanga ndiwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga mmene zililimu, si inenso mwini amene ndimazichita zimenezi, koma tchimo limene lili mʼkati mwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsopano si ine ndicicita, koma ucimo wakukhalabe m'kati mwanga ndiwo.