Romans 7:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanga umakondwa ndi Malamulo a Mulungu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti monga mwa munthu wa m'kati mwanga, ine ndikondwera ndi chilamulo cha Mulungu:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wanga umakondwera ndi lamulo la Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti monga mwa munthu wa m'kati mwanga, ine ndikondwera ndi cilamulo ca Mulungu: