Romans 7:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha lamuloli, uchimo udapeza mpata woutsa mwa ine khalidwe la masiriro osiyanasiyana. Pakuti ngati palibe malamulo, uchimo sungachite kanthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma uchimo, pamene unapeza chifukwa, unachita m'kati mwanga zilakolako zonse mwa lamulo; pakuti popanda lamulo uchimo uli wakufa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma chifukwa cha Malamulo uchimo unapeza mwayi owutsa mʼkati mwanga khalidwe lililonse la kusirira. Pakuti pakanapanda Malamulo, uchimo ukanakhala wopanda mphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma ucimo, pamene unapeza cifukwa, unacita m'kati mwanga zilakolako zonse mwa lamulo; pakuti popanda lamulo ucimo uli wakufa.