Romans 7:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine kale ndinali ndi moyo opanda malamulo. Koma pamene ndidayamba kudziŵa malamulo, pomwepo uchimo udayamba kulimba,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kale ine ndinali wamoyo popanda lamulo; koma pamene lamulo linadza, uchimo unatsitsimuka, ndipo ine ndinafa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi ina ndinali ndi moyo popanda Malamulo. Koma nditayamba kudziwa Malamulo, pomwepo uchimo unayamba kuphuka,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kale ine ndinali wamoyo popanda lamulo; koma pamene lamulo linadza, ucimo unatsitsimuka, ndipo ine ndinafa.