Romans 8:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati tiyembekeza zimene sitidaziwone ndi maso, timazidikira mopirira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati tiyembekezera chimene sitichipenya, pomwepo tichilindirira ndi chipiriro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati ife tiyembekeza chimene tikanalibe, ndiye kuti tikuyembekeza modekha mtima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati tiyembekezera cimene: siticipenya, pomwepo ticilindirira ndi cipiriro.