Romans 8:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndani angaŵaimbe mlandu anthu amene Mulungu adaŵasankha? Mulungu mwiniwake amaŵaona kuti ngolungama pamaso pake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndani adzaneneza osankhidwa a Mulungu? Mulungu ndiye amene awayesa olungama;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndani amene adzabweretsa mlandu kutsutsa amene Mulungu anawasankha? Ndi Mulungu amene amalungamitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndani adzaneneza osankhidwa a Mulungu? 8 Mulungu ndiye ameneawayesa olungama;