Romans 8:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Malembo akuti, “Chifukwa cha Inu tsiku lonse akufuna kutipha, pamaso pao tili ngati nkhosa zimene akukazipha.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monganso kwalembedwa, Chifukwa cha Inu tilikuphedwa dzuwa lonse; tinayesedwa monga nkhosa zakupha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga kwalembedwa: “Chifukwa cha inu, ife tikuphedwa tsiku lonse: ife tikutengedwa ngati nkhosa zoti zikaphedwe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monganso kwalembedwa, 12 Cifukwa ca Inu tirikuphedwa dzuwa lonse; Tinayesedwa monga nkhosa zakupha,