Romans 9:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo si pokhapo ai. Ana aŵiri a Rebeka aja bambo wao anali mmodzi, kholo lathu Isaki.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo si chotero chokha, koma Rebekanso, pamene anali ndi pakati pa mmodzi, ndiye kholo lathu Isaki;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo si pokhapo ayi. Ana awiri a Rebeka aja abambo awo anali mmodzi, kholo lathu Isake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo si cotero cokha, koma Rebekanso, pamene anali ndi pakati pa mmodzi, ndiye kholo lathu Isake;